Mayi Wina Watopa ndikugonana ndi Ndondocha
Mvangeli Online Mvangeli Online
304 subscribers
6,476 views
104

 Published On Mar 12, 2023

Mverani program ya Zilipati yokhudza nkhani ya mayi wina ku Blantyre yemwe akuulura kuti watopa ndikusamalira ndondocha zomwe mamuna wake anakatenga kwa sing'anga wina ku Mozambique kuti alemere.

Mwa zina mayi-yu wauza Zilipati kuti amauzidwa kuti azigonana ndi ndondocha yaimuna ndipo mamuna wake azigonana ndi ndondocha yaikazi

Iye wauzaso Zilipati kuti anauzidwa kuti aphe mwana wawo mmodzi komanso adzipha wachibale chaka chilichonse.
Programuyi inagulitsidwa pa #MIJ FM pa program ya #zilipati, ife a Mvangeli Online tiilibe umwini pa video imeyi.

show more

Share/Embed